Salimo 140:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anola lilime lawo ndipo lakhala ngati la njoka.+M’milomo yawo muli poizoni wa mphiri.+ [Seʹlah.]