Aroma 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Mmero wawo* ndi manda otseguka. Iwo amalankhula zachinyengo ndi lilime lawo.”+ “Mʼmilomo yawo muli poizoni wa njoka.”+ Yakobo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma palibe munthu amene angathe kuweta lilime. Lilime ndi losalamulirika ndipo limavulaza komanso ndi lodzaza ndi poizoni wakupha.+
13 “Mmero wawo* ndi manda otseguka. Iwo amalankhula zachinyengo ndi lilime lawo.”+ “Mʼmilomo yawo muli poizoni wa njoka.”+
8 Koma palibe munthu amene angathe kuweta lilime. Lilime ndi losalamulirika ndipo limavulaza komanso ndi lodzaza ndi poizoni wakupha.+