Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Nditetezeni ngati mwana wa diso lanu,+

      Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu.+

  • Salimo 36:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Musalole kuti phazi la anthu odzikweza lindipondereze

      Kapena kuti dzanja la anthu oipa lindithamangitse.

  • Salimo 71:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Inu Mulungu wanga, ndipulumutseni mʼmanja mwa woipa,+

      Kuti ndisagwidwe ndi munthu wochita zinthu mopondereza komanso wopanda chilungamo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena