Salimo 17:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nditetezeni ngati mwana wa diso lanu,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu.+ 9 Nditetezeni kwa anthu oipa amene akundiukira,Kwa adani* ochokera kufumbi amene andizungulira.+ Salimo 59:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Inu Mulungu wanga, ndipulumutseni kwa adani anga.+Nditetezeni kwa anthu amene akundiukira.+ Salimo 140:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Yehova, nditetezeni kuti manja a munthu woipa asandikhudze.+Nditetezeni kwa anthu amene amachita zachiwawa.Amene amakonza chiwembu kuti andivulaze. Mateyu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tithandizeni kuti tisagonje tikamayesedwa,*+ koma mutiteteze kwa woipayo.’+
8 Nditetezeni ngati mwana wa diso lanu,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu.+ 9 Nditetezeni kwa anthu oipa amene akundiukira,Kwa adani* ochokera kufumbi amene andizungulira.+
4 Inu Yehova, nditetezeni kuti manja a munthu woipa asandikhudze.+Nditetezeni kwa anthu amene amachita zachiwawa.Amene amakonza chiwembu kuti andivulaze.