Salimo 140:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Yehova, ndithandizeni kuti manja a munthu woipa asandikhudze.+Nditetezeni kwa munthu wochita zachiwawa.+Nditetezeni kwa anthu amene andikonzera chiwembu kuti andikankhe ndi kundigwetsa.+
4 Inu Yehova, ndithandizeni kuti manja a munthu woipa asandikhudze.+Nditetezeni kwa munthu wochita zachiwawa.+Nditetezeni kwa anthu amene andikonzera chiwembu kuti andikankhe ndi kundigwetsa.+