Salimo 21:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, mfumu ikusangalala chifukwa mwasonyeza kuti ndinu wamphamvu.+Ikusangalala kwambiri chifukwa mwaipulumutsa.+ 2 Mwaipatsa zimene mtima wake umalakalaka,+Ndipo simunaimane zopempha za milomo yake. (Selah)
21 Inu Yehova, mfumu ikusangalala chifukwa mwasonyeza kuti ndinu wamphamvu.+Ikusangalala kwambiri chifukwa mwaipulumutsa.+ 2 Mwaipatsa zimene mtima wake umalakalaka,+Ndipo simunaimane zopempha za milomo yake. (Selah)