Salimo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tandipempha, ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kuti ikhale cholowa chako,Ndiponso dziko lonse lapansi kuti likhale lako.+ Salimo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akupatseni zimene mtima wanu umalakalaka+Ndipo achititse kuti mapulani anu onse ayende bwino.*
8 Tandipempha, ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kuti ikhale cholowa chako,Ndiponso dziko lonse lapansi kuti likhale lako.+