Oweruza 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe,+Koma amene amakukondani awale ngati mmene dzuwa limawalira likamatuluka.” Ndipo dzikolo linakhala pa mtendere kwa zaka 40.+ Salimo 125:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 125 Anthu amene amakhulupirira Yehova+Ali ngati phiri la Ziyoni, limene silingagwedezekeKoma lidzakhalapo mpaka kalekale.+
31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe,+Koma amene amakukondani awale ngati mmene dzuwa limawalira likamatuluka.” Ndipo dzikolo linakhala pa mtendere kwa zaka 40.+
125 Anthu amene amakhulupirira Yehova+Ali ngati phiri la Ziyoni, limene silingagwedezekeKoma lidzakhalapo mpaka kalekale.+