1 Mafumu 8:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyo Solomo ananena kuti: “Yehova anati adzakhala mumdima wandiweyani.+ 13 Ine ndakwanitsa kukumangirani nyumba yapamwamba yomwe ndi malo okhazikika oti muzikhalamo mpaka kalekale.”+ Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili mʼdera lakutali lakumpoto,Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka komanso anthu padziko lonse lapansi akusangalala nalo,+Ndipo ndi mzinda wa Mfumu Yaikulu.+ Salimo 132:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+ 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka kalekale.Ndidzakhala mmenemu,+ chifukwa zimenezi ndi zimene ndikulakalaka.
12 Pa nthawiyo Solomo ananena kuti: “Yehova anati adzakhala mumdima wandiweyani.+ 13 Ine ndakwanitsa kukumangirani nyumba yapamwamba yomwe ndi malo okhazikika oti muzikhalamo mpaka kalekale.”+
2 Phiri la Ziyoni limene lili mʼdera lakutali lakumpoto,Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka komanso anthu padziko lonse lapansi akusangalala nalo,+Ndipo ndi mzinda wa Mfumu Yaikulu.+
13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+ 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka kalekale.Ndidzakhala mmenemu,+ chifukwa zimenezi ndi zimene ndikulakalaka.