Salimo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale ndikuyenda mʼchigwa chamdima wandiweyani,+Sindikuopa kanthu,+Chifukwa inu muli ndi ine.+Chibonga chanu ndi ndodo yanu zikundipangitsa kumva kuti ndine wotetezeka.* Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pamenepa? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+ Aheberi 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tikhale olimba mtima ndithu ndipo tinene kuti: “Yehova* ndi amene amandithandiza. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+
4 Ngakhale ndikuyenda mʼchigwa chamdima wandiweyani,+Sindikuopa kanthu,+Chifukwa inu muli ndi ine.+Chibonga chanu ndi ndodo yanu zikundipangitsa kumva kuti ndine wotetezeka.*
6 Tikhale olimba mtima ndithu ndipo tinene kuti: “Yehova* ndi amene amandithandiza. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+