Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 65:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Wosangalala ndi munthu amene inu mwamusankha nʼkumubweretsa pafupi ndi inu,

      Kuti akhale mʼmabwalo anu.+

      Tidzakhutira ndi zinthu zabwino zamʼnyumba yanu,+

      Kachisi wanu woyera.*+

  • Salimo 135:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ya wasankha Yakobo kuti akhale wake,

      Wasankha Isiraeli kuti akhale chuma chake chapadera.*+

  • 1 Petulo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma inu ndi “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera+ ndiponso anthu oti adzakhale chuma chapadera.+ Mwasankhidwa kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a Mulungu amene anakuitanani kuti muchoke mumdima ndipo anakulandirani mʼkuwala kwake kodabwitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena