Mlaliki 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa munthu wanzeru komanso munthu wopusa,+ onsewa sadzakumbukiridwa mpaka kalekale. Mʼmasiku amene akubwerawa aliyense adzaiwalika. Ndipo kodi wanzeru adzafa bwanji? Adzafa mofanana ndi wopusa.+ Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uchimo unalowa mʼdziko kudzera mwa munthu mmodzi ndipo uchimowo unabweretsa imfa.+ Choncho imfayo inafalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa . . .+
16 Chifukwa munthu wanzeru komanso munthu wopusa,+ onsewa sadzakumbukiridwa mpaka kalekale. Mʼmasiku amene akubwerawa aliyense adzaiwalika. Ndipo kodi wanzeru adzafa bwanji? Adzafa mofanana ndi wopusa.+
12 Uchimo unalowa mʼdziko kudzera mwa munthu mmodzi ndipo uchimowo unabweretsa imfa.+ Choncho imfayo inafalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa . . .+