Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 141:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+

      Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+

      Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+

      Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.

  • Miyambo 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mwana wanzeru amalandira malangizo* ochokera kwa bambo ake,+

      Koma wonyoza samvera akadzudzulidwa.*+

  • Aheberi 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nʼzoona kuti palibe chilango chimene chimakhala chosangalatsa pa nthawi yomwe ukuchilandira, koma chimakhala chowawa. Komabe pambuyo pake, kwa anthu amene aphunzirapo kanthu pa chilangocho, chimabala chipatso chamtendere, chomwe ndi chilungamo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena