Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe. Pemphero lopembedzera la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.*+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+ 1 Yohane 3:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Okondedwa, ngati mitima yathu sikutitsutsa, tikhoza kulankhula momasuka ndi Mulungu.+ 22 Ndipo chilichonse chimene tingamupemphe adzatipatsa,+ chifukwa timamvera malamulo ake komanso tikuchita zinthu zomusangalatsa.
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe. Pemphero lopembedzera la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.*+
12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+
21 Okondedwa, ngati mitima yathu sikutitsutsa, tikhoza kulankhula momasuka ndi Mulungu.+ 22 Ndipo chilichonse chimene tingamupemphe adzatipatsa,+ chifukwa timamvera malamulo ake komanso tikuchita zinthu zomusangalatsa.