Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu amene sakwiya msanga ndi wozindikira zinthu kwambiri,+Koma wosaugwira mtima amasonyeza uchitsiru wake.+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense azikhala wokonzeka kumvetsera, aziganiza kaye asanalankhule+ komanso asamafulumire kukwiya,+
29 Munthu amene sakwiya msanga ndi wozindikira zinthu kwambiri,+Koma wosaugwira mtima amasonyeza uchitsiru wake.+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense azikhala wokonzeka kumvetsera, aziganiza kaye asanalankhule+ komanso asamafulumire kukwiya,+