1 Samueli 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Popeza kuti Yonatani, mwana wa Sauli, ankakonda kwambiri Davide,+ iye anauza Davide kuti: “Bambo anga akufuna kukupha. Chonde mawa mʼmawa usamale. Udzapite kukabisala ndipo ukakhale komweko. 1 Samueli 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Yonatani analankhula zabwino za Davide+ kwa Sauli bambo ake. Iye anawauza kuti: “Mfumu isachimwire mtumiki wake Davide, chifukwa iye sanakulakwireni, ndipo wakhala akukuchitirani zinthu zabwino kwambiri. Miyambo 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mnzako weniweni amakusonyeza chikondi nthawi zonse,+Ndipo ndi mʼbale amene anabadwa kuti akuthandize pakagwa mavuto.+
2 Popeza kuti Yonatani, mwana wa Sauli, ankakonda kwambiri Davide,+ iye anauza Davide kuti: “Bambo anga akufuna kukupha. Chonde mawa mʼmawa usamale. Udzapite kukabisala ndipo ukakhale komweko.
4 Choncho Yonatani analankhula zabwino za Davide+ kwa Sauli bambo ake. Iye anawauza kuti: “Mfumu isachimwire mtumiki wake Davide, chifukwa iye sanakulakwireni, ndipo wakhala akukuchitirani zinthu zabwino kwambiri.
17 Mnzako weniweni amakusonyeza chikondi nthawi zonse,+Ndipo ndi mʼbale amene anabadwa kuti akuthandize pakagwa mavuto.+