Yakobo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabereka tchimo. Ndipo tchimo likachitika, limabweretsa imfa.+ 2 Petulo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zikanakhala bwino akanapanda kudziwa molondola njira ya chilungamo, kusiyana nʼkuidziwa bwinobwino kenako nʼkupatuka pa malamulo oyera omwe analandira.+
15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabereka tchimo. Ndipo tchimo likachitika, limabweretsa imfa.+
21 Zikanakhala bwino akanapanda kudziwa molondola njira ya chilungamo, kusiyana nʼkuidziwa bwinobwino kenako nʼkupatuka pa malamulo oyera omwe analandira.+