Miyambo 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi waona munthu amene amaganiza kuti ndi wanzeru?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu kuposa iyeyo. Aroma 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera. Musamaganize modzikuza, koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musamadzione ngati anzeru.+
12 Kodi waona munthu amene amaganiza kuti ndi wanzeru?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu kuposa iyeyo.
16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera. Musamaganize modzikuza, koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musamadzione ngati anzeru.+