Miyambo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wina* akutamande, osati pakamwa pako.Anthu ena* akutamande, osati milomo yako.+ Yohane 5:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mungakhulupirire bwanji pamene mukulandira ulemerero kuchokera kwa anthu anzanu, koma osayesetsa kuti mupeze ulemerero wochokera kwa Mulungu yekhayo?+ Afilipi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musamachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena chifukwa chodzikuza,+ koma modzichepetsa, muziona kuti ena amakuposani.+
44 Mungakhulupirire bwanji pamene mukulandira ulemerero kuchokera kwa anthu anzanu, koma osayesetsa kuti mupeze ulemerero wochokera kwa Mulungu yekhayo?+
3 Musamachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena chifukwa chodzikuza,+ koma modzichepetsa, muziona kuti ena amakuposani.+