Miyambo 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Si bwino kudya uchi wambiri,+Komanso si bwino kuti munthu adzifunire yekha ulemerero.+ Yeremiya 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitame chifukwa cha nzeru zake.+Munthu wamphamvu asadzitame chifukwa cha mphamvu zake.Ndipo munthu wachuma asadzitame chifukwa cha chuma chake.”+ 2 Akorinto 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa amene amavomerezedwa si wodzikweza,+ koma amene Yehova* wamuvomereza.+
23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitame chifukwa cha nzeru zake.+Munthu wamphamvu asadzitame chifukwa cha mphamvu zake.Ndipo munthu wachuma asadzitame chifukwa cha chuma chake.”+