Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:9-11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Tsiku linanso analota maloto ena, ndipo anauza abale akewo kuti: “Leronso ndinalota maloto ena. Ndinalota dzuwa ndi mwezi ndiponso nyenyezi zokwana 11 zikundigwadira.”+ 10 Kenako anafotokozeranso bambo ake ndi abale ake malotowo. Koma bambo ake anamʼdzudzula kuti: “Kodi maloto akowa akutanthauza chiyani? Kodi zoona ineyo ndi mayi akowa, komanso abale akowa tidzagwada pansi pamaso pa iwe?” 11 Abale akewo anamuchitira nsanje,+ koma bambo ake anasunga mawuwo mumtima.

  • Miyambo 14:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Mtima wodekha umapangitsa kuti thupi likhale lathanzi,

      Koma nsanje imawoletsa mafupa.+

  • Machitidwe 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma Ayuda anachita nsanje+ ndipo anasonkhanitsa anthu ena oipa amene ankangokhala pamsika. Iwowa anapanga gulu lachiwawa nʼkuyambitsa chipolowe mumzindamo. Kenako anapita kunyumba ya Yasoni, kukafuna Paulo ndi Sila kuti awatulutse nʼkuwapereka ku gulu limene linkachita chipolowelo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena