Salimo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzagona pansi nʼkupeza tulo,Ndipo ndidzadzuka ndili wotetezeka,Chifukwa Yehova akupitiriza kundithandiza.+ Miyambo 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ukamayenda adzakutsogolera.Ukamagona adzakulondera.Ndipo ukadzuka, adzakuuza zochita.*
5 Ine ndidzagona pansi nʼkupeza tulo,Ndipo ndidzadzuka ndili wotetezeka,Chifukwa Yehova akupitiriza kundithandiza.+