Salimo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzagona pansi mwamtendere nʼkupeza tulo,+Chifukwa inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+ Miyambo 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ukagona sudzaopa chilichonse.+Udzagona ndithu, ndipo tulo tako tidzakhala tokoma.+
8 Ndidzagona pansi mwamtendere nʼkupeza tulo,+Chifukwa inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+