Salimo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzagona pansi nʼkupeza tulo,Ndipo ndidzadzuka ndili wotetezeka,Chifukwa Yehova akupitiriza kundithandiza.+ Miyambo 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ukagona sudzaopa chilichonse.+Udzagona ndithu, ndipo tulo tako tidzakhala tokoma.+ Miyambo 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chifukwa uzidzadalira kwambiri Yehova,+Ndipo adzateteza phazi lako kuti lisakodwe.+
5 Ine ndidzagona pansi nʼkupeza tulo,Ndipo ndidzadzuka ndili wotetezeka,Chifukwa Yehova akupitiriza kundithandiza.+