Miyambo 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Njira ya Yehova ndi malo achitetezo kwa munthu wopanda cholakwa,+Koma anthu ochita zoipa amawonongedwa mʼnjira imeneyi.+ Miyambo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,Koma olungama amakhala olimba mtima ngati mkango.*+
29 Njira ya Yehova ndi malo achitetezo kwa munthu wopanda cholakwa,+Koma anthu ochita zoipa amawonongedwa mʼnjira imeneyi.+