-
Maliko 4:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Iye anawauza kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi woti mumvetse chinsinsi chopatulika+ cha Ufumu wa Mulungu. Koma amene ali kunja amauzidwa zonse pogwiritsa ntchito mafanizo+ 12 kuti kuyangʼana, aziyangʼana ndithu koma asamaone. Kumva, azimva ndithu koma asamazindikire tanthauzo lake. Komanso kuti asatembenuke nʼkukhululukidwa.”+
-