Salimo 66:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati mumtima mwanga ndikanakhala ndi maganizo aliwonse oti ndichitire munthu zoipa,Yehova sakanandimvetsera.+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova ali kutali ndi anthu oipa,Koma amamva pemphero la anthu olungama.+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+
18 Ngati mumtima mwanga ndikanakhala ndi maganizo aliwonse oti ndichitire munthu zoipa,Yehova sakanandimvetsera.+
15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+