Miyambo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Phunzitsa mwana kuti aziyenda mʼnjira imene akuyenera kuyendamo.+Ngakhale akadzakalamba sadzachoka mʼnjira imeneyo.+ Miyambo 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uchitsiru umakhazikika mumtima mwa mwana.+Koma ndodo yomulangira ndi imene imauthamangitsira kutali ndi iye.+ Miyambo 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana usalephere kumupatsa chilango.*+ Ngakhale utamukwapula ndi chikwapu, sangafe. Aefeso 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu abambo, musamapsetse mtima ana anu,+ koma pitirizani kuwalera powapatsa malangizo*+ komanso kuwaphunzitsa mogwirizana ndi zimene Yehova* amanena.+
6 Phunzitsa mwana kuti aziyenda mʼnjira imene akuyenera kuyendamo.+Ngakhale akadzakalamba sadzachoka mʼnjira imeneyo.+
15 Uchitsiru umakhazikika mumtima mwa mwana.+Koma ndodo yomulangira ndi imene imauthamangitsira kutali ndi iye.+
4 Inu abambo, musamapsetse mtima ana anu,+ koma pitirizani kuwalera powapatsa malangizo*+ komanso kuwaphunzitsa mogwirizana ndi zimene Yehova* amanena.+