Genesis 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa nthawi yokolola tirigu, Rubeni+ anapita kutchire kukayenda. Kumeneko anapezako zipatso za mandereki,* ndipo anazitenga nʼkupita nazo kwa Leya mayi ake. Ndiyeno Rakele anapempha Leya kuti: “Chonde, undipatseko mandereki a mwana wakowa.”
14 Pa nthawi yokolola tirigu, Rubeni+ anapita kutchire kukayenda. Kumeneko anapezako zipatso za mandereki,* ndipo anazitenga nʼkupita nazo kwa Leya mayi ake. Ndiyeno Rakele anapempha Leya kuti: “Chonde, undipatseko mandereki a mwana wakowa.”