Genesis 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa nthawi yokolola tirigu,+ Rubeni+ anapita kutchire kukayenda. Kumeneko anapezako zipatso za mandereki,* ndipo anawatenga n’kupita nawo kwa Leya mayi ake. Ndiyeno Rakele anapempha Leya kuti: “Chonde, ndigawireko mandereki+ a mwana wakowa.” Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:14 Nsanja ya Olonda,10/1/2007, tsa. 111/15/2004, tsa. 28
14 Pa nthawi yokolola tirigu,+ Rubeni+ anapita kutchire kukayenda. Kumeneko anapezako zipatso za mandereki,* ndipo anawatenga n’kupita nawo kwa Leya mayi ake. Ndiyeno Rakele anapempha Leya kuti: “Chonde, ndigawireko mandereki+ a mwana wakowa.”