1 Akorinto 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chikondi sichitha. Koma kaya pali mphatso za kunenera, zidzatha. Kaya Kulankhula malilime,* kudzatha. Ngakhale mphatso yodziwa zinthu, idzatha. 1 Akorinto 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komabe, tsopano patsala zitatu izi: Chikhulupiriro, chiyembekezo ndi chikondi. Koma chachikulu pa zonsezi ndi chikondi.+
8 Chikondi sichitha. Koma kaya pali mphatso za kunenera, zidzatha. Kaya Kulankhula malilime,* kudzatha. Ngakhale mphatso yodziwa zinthu, idzatha.
13 Komabe, tsopano patsala zitatu izi: Chikhulupiriro, chiyembekezo ndi chikondi. Koma chachikulu pa zonsezi ndi chikondi.+