Nyimbo ya Solomo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwe njiwa yanga, amene uli mʼmalo obisika apathanthwe,+Amene uli mʼmingʼalu yamʼmalo otsetsereka,Ndikufuna ndikuone komanso kumva mawu ako,+Chifukwa mawu ako ndi osangalatsa ndipo iweyo ndiwe wokongola.’”+
14 Iwe njiwa yanga, amene uli mʼmalo obisika apathanthwe,+Amene uli mʼmingʼalu yamʼmalo otsetsereka,Ndikufuna ndikuone komanso kumva mawu ako,+Chifukwa mawu ako ndi osangalatsa ndipo iweyo ndiwe wokongola.’”+