Nyimbo ya Solomo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwe njiwa yanga,+ tuluka m’malo obisika a pathanthwe. Tuluka pamalo osaoneka m’mphepete mwa njira yotsetsereka. Ndikufuna ndione thupi lako lokongola.+ Ndikufuna kumva mawu ako, chifukwa mawu ako ndi okoma ndipo iweyo ndiwe wokongola.’”+
14 Iwe njiwa yanga,+ tuluka m’malo obisika a pathanthwe. Tuluka pamalo osaoneka m’mphepete mwa njira yotsetsereka. Ndikufuna ndione thupi lako lokongola.+ Ndikufuna kumva mawu ako, chifukwa mawu ako ndi okoma ndipo iweyo ndiwe wokongola.’”+