Nyimbo ya Solomo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Inu ana aakazi a ku Yerusalemu,+ ine ndine mtsikana wakuda ngati mahema a ku Kedara,+ koma wokongola ngati nsalu za mahema+ a Solomo. Nyimbo ya Solomo 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Kodi mkazi+ amene akuyang’ana pansi ngati m’bandakuchayu ndani,+ wokongola ngati mwezi wathunthu,+ wosadetsedwa ngati dzuwa lowala,+ wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera?’”+
5 “Inu ana aakazi a ku Yerusalemu,+ ine ndine mtsikana wakuda ngati mahema a ku Kedara,+ koma wokongola ngati nsalu za mahema+ a Solomo.
10 ‘Kodi mkazi+ amene akuyang’ana pansi ngati m’bandakuchayu ndani,+ wokongola ngati mwezi wathunthu,+ wosadetsedwa ngati dzuwa lowala,+ wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera?’”+