-
Nyimbo ya Solomo 8:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 “Ine ndine khoma,
Ndipo mabere anga ali ngati nsanja.
Choncho mʼmaso mwa wokondedwa wanga ndakhala
Ngati mkazi amene wapeza mtendere.
-