Nyimbo ya Solomo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ine ndine khoma, ndipo mabere anga ali ngati nsanja.+ Choncho m’maso mwake ndakhala ngati mkazi amene wapeza mtendere. Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:10 Galamukani!,3/8/1992, tsa. 10
10 “Ine ndine khoma, ndipo mabere anga ali ngati nsanja.+ Choncho m’maso mwake ndakhala ngati mkazi amene wapeza mtendere.