Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 44:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yehova, Wokuwombola+

      Ndiponso amene anakuumba kuyambira uli mʼmimba, wanena kuti:

      “Ine ndine Yehova amene ndinapanga chilichonse.

      Ndinatambasula ndekha kumwamba,+

      Ndipo ndinayala dziko lapansi.+

      Kodi ndi ndani amene anali ndi ine?

  • Yeremiya 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iye ndi Mulungu amene anapanga dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zake,

      Amene anakhazikitsa dziko lapansi pogwiritsa ntchito nzeru zake.+

      Amenenso anatambasula kumwamba chifukwa cha kuzindikira kwake.+

  • Zekariya 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Uthenga wokhudza Isiraeli:

      “Awa ndi mawu a Yehova okhudza Isiraeli.”

      Yehova, amene anatambasula kumwamba,+

      Amene anayala maziko a dziko lapansi,+

      Komanso amene anapanga mzimu* umene uli mwa munthu, wanena kuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena