Deuteronomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Muziopa Yehova Mulungu wanu+ nʼkumamutumikira,+ ndipo muzilumbira pa dzina lake.+ Aroma 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Malembatu amati: “‘Pali ine Mulungu wamoyo,’+ watero Yehova,* ‘bondo lililonse lidzandigwadira, ndipo lilime lililonse lidzavomereza poyera kuti ndine Mulungu.’”+
11 Malembatu amati: “‘Pali ine Mulungu wamoyo,’+ watero Yehova,* ‘bondo lililonse lidzandigwadira, ndipo lilime lililonse lidzavomereza poyera kuti ndine Mulungu.’”+