Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 22:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno mngelo wa Yehova anaitana Abulahamu kachiwiri kuchokera kumwamba,

  • Genesis 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbadwa* zako ngati nyenyezi zakumwamba komanso ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.+ Ndipo mbadwa yako idzalanda mzinda* wa adani ake.+

  • Yeremiya 33:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ine ndidzachulukitsa mbadwa* za Davide mtumiki wanga ndi Alevi amene akunditumikira. Ndidzazichulukitsa mofanana ndi kuchuluka kwa nyenyezi zonse zakumwamba* zimene sizingawerengedwe ndiponso mofanana ndi mchenga umene sungayezedwe.’”

  • Hoseya 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipo Aisiraeli* adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene ankauzidwa kuti, ‘Siinu anthu anga,’+ adzauzidwa kuti, ‘Ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena