2 Akorinto 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Choncho chokani pakati pawo ndipo musiyane nawo,’ watero Yehova.* ‘Musakhudze chinthu chodetsedwa,’”+ “‘ndipo ndidzakulandirani.’”+ Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinamva mawu ena kuchokera kumwamba akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.+
17 “‘Choncho chokani pakati pawo ndipo musiyane nawo,’ watero Yehova.* ‘Musakhudze chinthu chodetsedwa,’”+ “‘ndipo ndidzakulandirani.’”+
4 Ndinamva mawu ena kuchokera kumwamba akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.+