Yesaya 52:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chokanimo, chokanimo, tulukani mmenemo,+ musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa!+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera,Inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+ Yeremiya 51:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Tulukani mʼBabulo anthu anga.+ Thawani mkwiyo wa Yehova+ woyaka moto kuti mupulumutse moyo wanu.+ Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinamva mawu ena kuchokera kumwamba akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.+
11 Chokanimo, chokanimo, tulukani mmenemo,+ musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa!+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera,Inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+
4 Ndinamva mawu ena kuchokera kumwamba akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.+