Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ azikumbukira kuti ndine woyera, ndipo anthu onse adzandipatsa ulemerero.’” Koma Aroni anangokhala chete.

  • Numeri 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+

  • Numeri 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Azisamalira ziwiya zonse+ zapachihema chokumanako, komanso kukwaniritsa udindo wawo wotumikira Aisiraeli pogwira ntchito zapachihema.+

  • Ezara 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mfumu Koresi inabweretsanso ziwiya zamʼnyumba ya Yehova. Ziwiyazo nʼzimene Nebukadinezara anatenga ku Yerusalemu nʼkukaziika mʼkachisi wa mulungu wake.+

  • Ezara 8:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ansembe ndi Aleviwo analandira siliva ndi golide amene anayezedwayo ndiponso ziwiya zimene zinayezedwazo, kuti apititse zinthuzi ku Yerusalemu kunyumba ya Mulungu wathu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena