Numeri 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Utenge Alevi pakati pa Aisiraeli ndipo uwayeretse.+ Numeri 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Utengenso abale ako a fuko la Levi, omwe ndi a mtundu wa bambo ako, kuti azikuthandiza. Azitumikira iweyo+ limodzi ndi ana ako pachihema cha Umboni.+
2 Utengenso abale ako a fuko la Levi, omwe ndi a mtundu wa bambo ako, kuti azikuthandiza. Azitumikira iweyo+ limodzi ndi ana ako pachihema cha Umboni.+