Ekisodo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ubweretse Aroni ndi ana ake pakhomo la chihema chokumanako,+ ndipo uwasambitse* ndi madzi.+ Yesaya 52:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chokanimo, chokanimo, tulukani mmenemo,+ musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa!+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera,Inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+
11 Chokanimo, chokanimo, tulukani mmenemo,+ musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa!+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera,Inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+