Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+

  • Numeri 8:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno Aleviwo analowa mʼchihema chokumanako nʼkukayamba utumiki wawo pamaso pa Aroni ndi ana ake. Anthu anachitira Aleviwo mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose zokhudza Alevi.

  • Numeri 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kodi mukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti Mulungu wa Isiraeli anakupatulani pakati pa Aisiraeli,+ nʼkukulolani kuti muzifika pamaso pa Yehova kuti muzimutumikira pachihema chake komanso kutumikira gulu lonselo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena