Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,

      Ndipo anthu olemekezeka asonkhana pamodzi* mogwirizana+

      Kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.*+

  • Salimo 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Amene wakhala pampando wachifumu kumwamba adzaseka.

      Yehova adzawanyogodola.

  • Yesaya 41:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu amene akulimbana nawe udzawafunafuna koma sudzawapeza.

      Anthu amene akumenyana nawe adzakhala ngati chinthu chimene kulibeko ndipo sadzakhalanso ngati kanthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena