Yeremiya 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼmasiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Isiraeli adzakhala motetezeka.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala: Yehova Ndi Chilungamo Chathu.”+
6 Mʼmasiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Isiraeli adzakhala motetezeka.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala: Yehova Ndi Chilungamo Chathu.”+