Yesaya 60:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Alendo adzamanga mipanda yako,Ndipo mafumu awo adzakutumikira.+Ine ndinakulanga chifukwa ndinali nditakwiya,Koma chifukwa cha kukoma mtima kwanga* ndidzakuchitira chifundo.+ Zekariya 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Mʼmasiku amenewo, amuna 10 ochokera mʼzilankhulo zonse za anthu a mitundu ina+ adzagwira mkanjo* wa Myuda nʼkunena kuti: “Anthu inu tikufuna tipite nanu limodzi,+ chifukwa tamva kuti Mulungu ali ndi inu.”’”+
10 Alendo adzamanga mipanda yako,Ndipo mafumu awo adzakutumikira.+Ine ndinakulanga chifukwa ndinali nditakwiya,Koma chifukwa cha kukoma mtima kwanga* ndidzakuchitira chifundo.+
23 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Mʼmasiku amenewo, amuna 10 ochokera mʼzilankhulo zonse za anthu a mitundu ina+ adzagwira mkanjo* wa Myuda nʼkunena kuti: “Anthu inu tikufuna tipite nanu limodzi,+ chifukwa tamva kuti Mulungu ali ndi inu.”’”+