Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Maso anu akhale akuyangʼana nyumba ino masana komanso usiku. Akhale akuyangʼana malo amene munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala kumeneko,’+ kuti mumvetsere pemphero limene mtumiki wanu angapemphere atayangʼana kumalo ano.+

  • 1 Mafumu 8:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 inuyo mumve muli kumwambako, kumene mumakhala,+ ndipo muchite zonse zimene mlendoyo wakupemphani. Muchite zimenezi kuti anthu a mitundu yonse yapadziko lapansi adziwe dzina lanu ndiponso akuopeni+ ngati mmene anthu anu Aisiraeli amachitira, komanso adziwe kuti dzina lanu lili panyumba imene ndamangayi.

  • Mateyu 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iye anawauza kuti: “Malemba amati, ‘Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo,’+ koma inu mukuisandutsa phanga la achifwamba.”+

  • Maliko 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iye ankaphunzitsa ndipo ankauza anthuwo kuti: “Kodi Malemba sanena kuti, ‘Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo anthu a mitundu yonseʼ?+ Koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+

  • Luka 19:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 nʼkuwauza kuti: “Malemba amati, ‘Nyumba yanga idzakhala nyumba yopemphereramo,’+ koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena