Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tsoka kwa anthu amene amatchuka ndi kumwa vinyo kwambiri,

      Komanso kwa anthu amene ndi akatswiri odziwa kusakaniza mowa.+

  • Yesaya 28:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Amenewanso asochera chifukwa cha vinyo.

      Akuyenda modzandira chifukwa cha mowa.

      Wansembe ndi mneneri asochera chifukwa cha mowa.

      Vinyo wawasokoneza,

      Ndipo akuyenda modzandira chifukwa cha mowa.

      Sakuona bwinobwino ndipo akusochera,

      Komanso akulephera kusankha zinthu mwanzeru.+

  • Hoseya 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chiwerewere, vinyo wakale ndiponso vinyo watsopano

      Zimalepheretsa munthu kuchita zoyenera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena